Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 23:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Paulo anati kwa iye, Mulungu adzakupanda iwe, khoma loyeretsedwa iwe; ndipo kodi ukhala iwe wakundiweruza mlandu monga mwa cilamulo, ndipo ulamulira andipande ine posanga cilamulo?

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 23

Onani Macitidwe 23:3 nkhani