Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 22:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndipo iwo amene anati amfunsefunse, anamsiya; ndipo kapitao wamkurunso anaopa, pozindikira kuti ndiye Mroma, ndiponso popeza adammanga iye.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 22

Onani Macitidwe 22:29 nkhani