Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 21:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

amenewa uwatenge nudziyeretse nao pamodzi, nuwalipirire, kati amete mutu; ndipo adzadziwa onse kuti zomveka za iwe nzacabe, koma kuti iwe wekhaoso uyenda molunjika, nusunga cilamulo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 21

Onani Macitidwe 21:24 nkhani