Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 21:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo kunali, titalekana nao ndi kukankha ngalawa, tinadza molunjika ku Ko, ndi m'mawa mwace ku Rode, ndipo pocokerapo ku Patara;

2. ndipo m'mene tinapeza ngalawa Yakuoloka kunka ku Foinike, tinalowamo, ndi kupita nayo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 21