Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 21:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, titalekana nao ndi kukankha ngalawa, tinadza molunjika ku Ko, ndi m'mawa mwace ku Rode, ndipo pocokerapo ku Patara;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 21

Onani Macitidwe 21:1 nkhani