Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 19:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati Paulo, Yohane anabatiza ndi ubatizo wa kutembenuka mtima, nati kwa anthu, kuti amkhulupirire iye amene adzadza pambuyo pace, ndiye Yesu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 19

Onani Macitidwe 19:4 nkhani