Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 19:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo tiopa ife kuti nchito yathuyi idzayamba kunyonyosoka; komanso kuti kacisi wa mlungu wamkazi Artemi adzayamba kuyesedwa wacabe; ndiponso kuti iye adzayamba kutsitsidwa ku ukulu wace, iye amene a m'Asiya onse, ndi onse a m'dziko lokhalamo anthu, ampembedza.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 19

Onani Macitidwe 19:27 nkhani