Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 18:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pamene Sila ndi Timoteo anadza potsika ku Makedoniya, Paulo anapsinjidwa ndi mau, nacitira umboni kwa Ayuda kuti Yesu ndiye Kristu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 18

Onani Macitidwe 18:5 nkhani