Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 18:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Paulo atakhala cikhalire masiku ambiri, anatsazika abale, nacoka pamenepo, napita m'ngalawa ku Suriya, pamodzi naye Priskila ndi Akula; popeza anameta mutu wace m'Kenkreya; pakuti adawinda.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 18

Onani Macitidwe 18:18 nkhani