Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 17:32-34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

32. Ndipo pamene anamva za kuuka kwa akufa ena anaseka pwepwete; koma ena anati, Tidzakumvanso za cimeneci.

33. Conco Paulo anaturuka pakati pao.

34. Koma ena anadziphatika kwa iye, nakhulupira; mwa iwonso munali Dionisiyo Mareopagi, ndi mkazi dzina lace Damarisi, ndi ena pamodzi nao.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 17