Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 17:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa anapangira tsiku limene adzaweruza dziko lokhalamo anthu m'cilungamo, ndi munthu amene anamuikiratu; napatsa anthu onse citsimikizo, pamene anamuukitsa iye kwa akufa.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 17

Onani Macitidwe 17:31 nkhani