Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 13:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene anapitirira cisumbu conse kufikira Pafo, anapezapo munthu watsenga, mneneri wonyenga, ndiye Myuda, dzina lace Baryesu;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 13

Onani Macitidwe 13:6 nkhani