Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 12:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mngelo anati kwa iye, Dzimangire m'cuuno, numange nsapato zako. Nacita cotero. Ndipo ananena naye, Pfunda cobvala cako, nunelitsate ine.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 12

Onani Macitidwe 12:8 nkhani