Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 12:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene adapitirira podikira poyamba ndi paciwiri, anadza ku citseko cacitsulo cakuyang'ana kumudzi; cimene cidawatsegukira cokha; ndipo anaturuka, napitirira khwalala limodzi; ndipo pomwepo mngelo anamcokera.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 12

Onani Macitidwe 12:10 nkhani