Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 11:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo m'mene anampeza, anadza naye ku Antiokeya. Ndipo kunali, kuti caka conse anasonkhana pamodzi mu Mpingo, naphunzitsa anthu aunyinji; ndipo ophunzira anayamba kuchedwa Akristu ku Antiokeya.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 11

Onani Macitidwe 11:26 nkhani