Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 11:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma panali ena mwa iwo, amuna a ku Kupro, ndi Kurene, amenewo, m'mene adafika ku Antiokeya, analankhula ndi Ahelene, ndi kulalikira Uthenga Wabwino wa Ambuye Yesu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 11

Onani Macitidwe 11:20 nkhani