Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 9:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye, m'mene anatenga mikate isanu ija ndi nsomba ziwiri anayang'ana kumwamba, nazidalitsa, nanyema, napatsa ophunzira apereke kwa anthuwo.

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:16 nkhani