Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 9:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atabwera atumwi, anamfotokozera iye zonse anazicita. Ndipo iye anawatenga, napatuka nao pa okha kunka ku mudzi dzina lace Betsaida.

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:10 nkhani