Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 8:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ataturuka pamtanda iye, anakomana naye mwamuna wa kumudzi, amene anali nazo ziwanda; ndipo masiku ambiri sanabvala cobvala, nisanakhala m'nyumba, koma m'manda.

Werengani mutu wathunthu Luka 8

Onani Luka 8:27 nkhani