Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 6:49 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iye amene akumva, ndi kusacita, afanafana ndi munthu wakumanga nyumba pa nthaka yopanda maziko; pa imeneyo unagunda mtsinje, ndipo inagwa pomwepo; ndipo kugumuka kwace kwa nyumbayo kunali kwakukuru.

Werengani mutu wathunthu Luka 6

Onani Luka 6:49 nkhani