Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 6:48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye afanafana ndi munthu wakumanga nyumba, amene anakumba pansi ndithu, namanga maziko a nyumbayo pathanthwe; ndipo pamene panadza cigumula, mtsinje unagunda pa nyumbayo, ndipo sunakhoza kuigwedeza; cifukwa idamangika bwino.

Werengani mutu wathunthu Luka 6

Onani Luka 6:48 nkhani