Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 6:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anatsika nao, naima pacidikha, ndi khamu lalikuru la ophunzira ace, nw unyinji waukuru wa anthu a ku Yudeya lonse ndi Yerusalemu, ndi a ku mbali ya nyanja ya ku Turo ndi Sidoni, amene anadza kudzamva iye ndi kudzaciritsidwa nthenda zao;

Werengani mutu wathunthu Luka 6

Onani Luka 6:17 nkhani