Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 5:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Afarisi ndi alembi ao anang'ung'udza kwa ophunzira ace nanena, kuti, Bwanji inu mukudya ndi kumwa pamodzi ndi anthu amisonkho ndi ocimwa?

Werengani mutu wathunthu Luka 5

Onani Luka 5:30 nkhani