Ndipo Levi anamkonzera iye phwando lalikuru kunyumba kwace; ndipo panali khamu lalikuru la amisonkho, ndi enanso amene analikuseama pacakudya pamodzi nao.