Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 3:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo Mzimu Woyera anatsika ndi maonekedwe a thupi lace ngati nkhunda, nadza pa iye; ndipo munaturuka mau m'thambo, kuti, Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa, mwa Iwe ndikondwera.

Werengani mutu wathunthu Luka 3

Onani Luka 3:22 nkhani