Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 16:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anakweza mau nati, Atate Abrahamu, mundicitire cifundo, mutome Lazaro, kuti abviike nsonga ya cala cace m'madzi, naziziritse lilime langa; pakuti ndizunzidwadi m'lawi ili la moto.

Werengani mutu wathunthu Luka 16

Onani Luka 16:24 nkhani