Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 13:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye ananena fanizo ili: Munthu wina anali ndi mkuyu wookam'munda wace wamphesa. Ndipo anadza nafuna cipatso pa uwu, koma anapeza palibe.

Werengani mutu wathunthu Luka 13

Onani Luka 13:6 nkhani