Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 13:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene atauka mwini nyumba natseka pakhomo, ndipo inu mudzayamba kuima pabwalo, ndi kugogoda pacitseko, ndi kunena, Ambuye titsegulireni ife; ndipo iye adzayankha nadzati ndi inu, Sindidziwa inu kumene mucokerako;

Werengani mutu wathunthu Luka 13

Onani Luka 13:25 nkhani