Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 12:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Gulitsani zinthu muli nazo, nimupatse mphatso zacifundo; mudzikonzere matumba a ndarama amene sakutha, cuma cosatha m'Mwamba, kumene mbala siziyandikira, ndipo njenjete siziononga.

Werengani mutu wathunthu Luka 12

Onani Luka 12:33 nkhani