Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 11:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amuna a ku Nineve adzaimirira pa mlandu wotsiriza pamodzi ndi anthu a mbadwo uno, nadzawatsutsa; pakuti iwo analapa pa kulalikira kwa Y ona; ndipo onani, wakuposa Y ona ali pano.

Werengani mutu wathunthu Luka 11

Onani Luka 11:32 nkhani