Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 11:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mfumu yaikazi ya kumwera idzaimirira pa mlandu wotsiriza pamodzi ndi amuna a mbadwo uno, nadzawatsutsa; pakuti anadza ku'cokera ku malekezero a dziko kudzamva nzeru za Solomo; ndipo onani, woposa Solomo ali pano.

Werengani mutu wathunthu Luka 11

Onani Luka 11:31 nkhani