Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 11:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pakunena izi iye, mkazi wina mwa khamu la anthu anakweza mau, nati kwa iye, Yodala mimba imene idakubalani, ndi mawere amene munayamwa.

Werengani mutu wathunthu Luka 11

Onani Luka 11:27 nkhani