Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 10:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zitatha izi Ambuye anaika ena makumi asanu ndi awiri, nawatuma iwo awiri awiri pamaso pace ku mudzi uli wonse, ndi malo ali onse kumene ati afikeko mwini.

Werengani mutu wathunthu Luka 10

Onani Luka 10:1 nkhani