Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 9:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapatsa ilo mphamvu si kuti likawaphe, komatu kuti likawazunze miyezi isanu; ndipo mazunzidwe ao anali ngati mazunzidwe a cinkhanira, pamene ciluma munthu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 9

Onani Cibvumbulutso 9:5 nkhani