Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 9:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo otsala a anthu osaphedwa nayo miliri iyo sanalapa nchito ya manja ao, kuti asapembedzere ziwanda, ndi mafano agolidi, ndi asiliva, ndi amkuwa, ndi amwala, ndi amtengo, amene sakhoza kupenya, kapena kumva, kapena kuyenda;

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 9

Onani Cibvumbulutso 9:20 nkhani