Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 8:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mngeloyo anatenga mbale ya zofukiza, naidzaza ndi mota wopara pa guwa la nsembe, nauponya pa dziko lapansi; ndipo panakhala mabingu, ndi mau, ndi mphezi, ndi cibvomezi.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 8

Onani Cibvumbulutso 8:5 nkhani