Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 8:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza mngelo wina, naima pa guwa la nsembe, nakhala naco cotengera ca zofukiza cagolidi; ndipo anampatsa zofukiza zambiri, kuti aziike pamodzi ndi mapemphero a oyera mtima onse pa guwa la nsembe lagolidi, lokhala ku mpando wacifumu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 8

Onani Cibvumbulutso 8:3 nkhani