Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 7:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinamva ciwerengo ca iwo osindikizidwa cizindikilo, zikwi makumi khumi ndi makumi anai mphambu anai, osindikizidwa cizindikilo mwa mafuko onse a ana a Israyeli,

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 7

Onani Cibvumbulutso 7:4 nkhani