Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 7:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinati kwa iye, Mbuye wanga, mudziwa ndinu. Ndipo anati kwaine, Iwo ndiwo akuturuka m'cisautso cacikuru; ndipo anatsuka zobvala zao, naziyeretsa m'mwazi wa Mwanawankhosa.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 7

Onani Cibvumbulutso 7:14 nkhani