Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 7:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mmodzi wa akuru anayankha, nanena ndi ine, Iwo obvala zobvala zoyera ndiwo ayani, ndipo acokera kuti?

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 7

Onani Cibvumbulutso 7:13 nkhani