Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 5:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo colengedwa ciri conse ciri m'mwamba, ndi padziko, ndi pansi pa dziko, ndi m'nyanja, ndi zonse ziri momwemo, ndinazimva zirikunena, Kwa iye wakukhala pa mpando wacifumu, ndi kwa Mwanawankhosa zikhale ciyamiko, ndi ulemu, ndi ulemerero, ndi ufumu, kufikira nthawi za nthawi.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 5

Onani Cibvumbulutso 5:13 nkhani