Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 5:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akunena ndi mau akulu, Ayenera Mwanawankhosa, wophedwayo, kulandira cilimbiko, ndi cuma, ndi nzeru, ndi mphamvu, ndi ulemu, ndi ulemerero, ndi ciyamiko.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 5

Onani Cibvumbulutso 5:12 nkhani