Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 4:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zamoyozo zinai, conse pa cokha cinali nao mapiko asanu ndi limodzi; ndipo zinadzala ndi maso pozinga ponse ndi m'katimo; ndipo sizipumula usana ndi usiku, ndi kunena, Woyera, woyera, woyera, Ambuye Mulungu Wamphamvuyonse, amene anali, amene ali, ndi amene alinkudza.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 4

Onani Cibvumbulutso 4:8 nkhani