Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 4:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo camoyo coyamba cinafanana nao mkango, ndi camoyo caciwiri cinafanana ndi mwana wa ng'ombe, ndi camoyo cacitatu cinali nayo nkhope yace ngati ya munthu, ndi camoyo cacinai cidafanana ndi ciombankhanga cakuuluka.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 4

Onani Cibvumbulutso 4:7 nkhani