Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 4:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akulu makumi awiri mphambu anai amagwa pansi pamaso pa iye wakukhala pa mpando wacifumu, namlambira iye amene akhala ndi moyo kufikira nthawi za nthawi, ndipo aponya pansi akorona ao ku mpando wacifumu, ndi kunena,

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 4

Onani Cibvumbulutso 4:10 nkhani