Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 22:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakati pa khwalala lace, ndi tsidya ili la mtsinje, ndi tsidya lace lija panali mtengo wa moyo wakubala zipatso khumi ndi ziwiri, ndi kupatsa zipatso zace mwezi ndi mwezi; ndipo masamba a mtengo ndiwo akuciritsa nao amitundu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 22

Onani Cibvumbulutso 22:2 nkhani