Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 21:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza mmodzi wa angelo asanu ndi awiri akukhala nazo mbale zisanu ndi ziwiri, zodzala ndi miliri yotsiriza isanu Ndi iwiri; ndipo analankhula ndi ine, nanena, Idza kuno, ndidzakuonetsa mkwatibwi, mkazi wa Mwanawankhosa.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 21

Onani Cibvumbulutso 21:9 nkhani