Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 21:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma amantha, ndi osakhulupira, ndi onyansa, ndi ambanda, ndi acigololo, ndi olambira mafano, ndi onse a mabodza, colandira cao cidzakhala m'nyanja yotentha ndi mota ndi sulfure; ndiyo imfa yaciwiri.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 21

Onani Cibvumbulutso 21:8 nkhani