Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 19:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinamva ngati mau a khamu lalikuru, ngati mkokomo wa madzi ambiri, ngati mau a mabingu olimba, nizinena, Aleluya; pakuti acita ufumu Ambuye Mulungu wathu, Wamphamvuyonse.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 19

Onani Cibvumbulutso 19:6 nkhani