Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 18:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Monga momwe unadzicitira ulemu, nudyerera, momwemo muucitire eouzunza ndi couliritsa maliro: pakuti unena mumtima mwace, Ndikhala ine mfumu, wosati wamasiye ine, wosaona maliro konse ine.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18

Onani Cibvumbulutso 18:7 nkhani